Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ziwiya zonse zagolide ndi zasiliva zinalipo 5,400 ndipo Sezibazara+ anabweretsa zonsezi ku Yerusalemu. Anatenganso anthu amene anagwidwa ukapolo+ kuchoka nawo ku Babulo n’kupita nawo ku Yerusalemu.

  • Ezara 7:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Munyamulenso siliva ndi golide yense amene mum’peze m’chigawo chonse cha Babulo, limodzi ndi mphatso za anthu+ ndi za ansembe omwe akupereka mwaufulu kunyumba ya Mulungu wawo,+ yomwe ili ku Yerusalemu.

  • Ezara 8:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ansembe ndi Aleviwo analandira siliva ndi golide amene anayezedwayo ndiponso ziwiya zimene zinayezedwazo, kuti apititse zinthuzi ku Yerusalemu kunyumba ya Mulungu wathu.+

  • Machitidwe 24:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho pambuyo pa zaka zambiri, ndinabwera kudzapatsa mtundu wanga mphatso zachifundo, ndiponso kudzapereka nsembe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena