Machitidwe 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chotero aliyense wa ophunzirawo, anatsimikiza mtima kutumiza thandizo+ lililonse limene akanatha+ kwa abale okhala ku Yudeya. 2 Akorinto 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndipo anapitiriza kutipempha mochokera pansi pa mtima ndiponso mochonderera kwambiri, kuti tiwapatse mwayi wopereka nawo mphatso zachifundo ndi kutinso achite nawo utumiki wothandiza oyerawo.+
29 Chotero aliyense wa ophunzirawo, anatsimikiza mtima kutumiza thandizo+ lililonse limene akanatha+ kwa abale okhala ku Yudeya.
4 ndipo anapitiriza kutipempha mochokera pansi pa mtima ndiponso mochonderera kwambiri, kuti tiwapatse mwayi wopereka nawo mphatso zachifundo ndi kutinso achite nawo utumiki wothandiza oyerawo.+