Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 28:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndipo ulowetse miyala iwiriyo pansalu za m’mapewa za efodi kuti ikhale miyala ya chikumbutso cha ana a Isiraeli.+ Poonekera kwa Yehova, Aroni azidzanyamula mayina awo pansalu ziwiri za m’mapewa ake kuti chikhale chikumbutso.

  • Yoswa 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Muzidzawauza kuti, ‘N’chifukwa chakuti madzi a mumtsinje wa Yorodano anadukana pamaso pa likasa la pangano la Yehova.+ Likasalo litadutsa mumtsinje wa Yorodano, madzi a mtsinje wa Yorodanowo anadukana, ndipo miyala imeneyi ndi chikumbutso cha zimenezo kwa ana a Isiraeli mpaka kalekale.’”*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena