Zekariya 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Galeta loyamba linali kukokedwa ndi mahatchi ofiira,+ ndipo galeta lachiwiri linali kukokedwa ndi mahatchi akuda.+ Zekariya 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mahatchi akuda amene akukoka galeta akupita kudziko la kumpoto.+ Mahatchi oyera akupita kutsidya la nyanja. Mahatchi amawangamawanga akupita kudziko la kum’mwera.+
2 Galeta loyamba linali kukokedwa ndi mahatchi ofiira,+ ndipo galeta lachiwiri linali kukokedwa ndi mahatchi akuda.+
6 Mahatchi akuda amene akukoka galeta akupita kudziko la kumpoto.+ Mahatchi oyera akupita kutsidya la nyanja. Mahatchi amawangamawanga akupita kudziko la kum’mwera.+