-
Danieli 7:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ndinayandikira mmodzi mwa amene anali ataimirira kuti ndimufunse tanthauzo la zonsezi.+ Choncho iye anandifotokozera kumasulira kwa nkhani zimenezi, kuti:
-