-
Danieli 7:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ndinayandikira mmodzi mwa amene anaimirira pamenepo kuti ndimufunse tanthauzo la zimenezi. Choncho iye anandifotokozera kumasulira kwa zinthu zimenezi. Iye anati:
-