Deuteronomo 28:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova adzakutsegulira kumwamba, nyumba yake yabwino yosungiramo zinthu, kuti akupatse mvula pa nyengo yake+ m’dziko lako ndi kuti adalitse ntchito iliyonse ya manja ako.+ Udzakongoza mitundu yambiri koma iwe sudzakongola kanthu kwa iwo.+ 2 Mafumu 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma msilikali wothandiza mfumu uja anamuyankha munthu wa Mulungu woonayo kuti: “Ngakhale Yehova atatsegula zotsekera madzi akumwamba, kodi mawu anuwa angakwaniritsidwe?”+ Pamenepo Elisa anati: “Uona zimenezi ndi maso ako, koma sudya nawo.”+
12 Yehova adzakutsegulira kumwamba, nyumba yake yabwino yosungiramo zinthu, kuti akupatse mvula pa nyengo yake+ m’dziko lako ndi kuti adalitse ntchito iliyonse ya manja ako.+ Udzakongoza mitundu yambiri koma iwe sudzakongola kanthu kwa iwo.+
19 Koma msilikali wothandiza mfumu uja anamuyankha munthu wa Mulungu woonayo kuti: “Ngakhale Yehova atatsegula zotsekera madzi akumwamba, kodi mawu anuwa angakwaniritsidwe?”+ Pamenepo Elisa anati: “Uona zimenezi ndi maso ako, koma sudya nawo.”+