Maliko 12:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pophunzitsapo Yesu ananenanso kuti: “Chenjerani ndi alembi+ amene amakonda kuyendayenda atavala mikanjo ndi kupatsidwa moni m’misika.
38 Pophunzitsapo Yesu ananenanso kuti: “Chenjerani ndi alembi+ amene amakonda kuyendayenda atavala mikanjo ndi kupatsidwa moni m’misika.