Aheberi 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musaiwale kuchereza alendo,+ pakuti potero, ena anachereza angelo mosadziwa.+ 3 Yohane 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wokondedwa, ukugwira ntchito mokhulupirika pa chilichonse chimene ukuchitira abale,+ amene sukuwadziwa n’komwe.+
5 Wokondedwa, ukugwira ntchito mokhulupirika pa chilichonse chimene ukuchitira abale,+ amene sukuwadziwa n’komwe.+