Maliko 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo akudya chakudya patebulo, Yesu anati: “Ndithu ndikukuuzani, Mmodzi wa inu, amene akudya+ nane limodzi, andipereka.”+ Yohane 6:70 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Pamenepo Yesu anati: “Ine ndinakusankhani inu 12,+ si choncho kodi? Komatu mmodzi wa inu ndi wonenera anzake zoipa.”+ Yohane 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Atanena zimenezi, Yesu anasautsika mu mzimu, ndipo anachitira umboni kuti: “Ndithudi ndikukuuzani, Mmodzi wa inu andipereka.”+
18 Ndipo akudya chakudya patebulo, Yesu anati: “Ndithu ndikukuuzani, Mmodzi wa inu, amene akudya+ nane limodzi, andipereka.”+
70 Pamenepo Yesu anati: “Ine ndinakusankhani inu 12,+ si choncho kodi? Komatu mmodzi wa inu ndi wonenera anzake zoipa.”+
21 Atanena zimenezi, Yesu anasautsika mu mzimu, ndipo anachitira umboni kuti: “Ndithudi ndikukuuzani, Mmodzi wa inu andipereka.”+