Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 22:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Iwo akugawana zovala zanga pakati pawo,+

      Ndipo akuchita maere pazovala zanga.+

  • Luka 23:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 [[Koma Yesu anati: “Atate, akhululukireni,+ chifukwa sakudziwa chimene akuchita.”]]* Ndipo iwo anagawana malaya ake mwa kuchita maere.+

  • Yohane 19:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Tsopano asilikaliwo atamupachika Yesu, anatenga malaya ake akunja ndi kuwagawa m’zigawo zinayi, kuti msilikali aliyense atenge chigawo chimodzi. Panalinso malaya amkati. Koma malaya amkatiwo analibe msoko, anali owombedwa kuchokera pamwamba mpaka pansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena