Maliko 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti mkatimo, mumtima mwa munthu,+ mumatuluka maganizo oipa. Mumatuluka zadama,*+ zakuba, zaumbanda,+ Maliko 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Zoipa zonsezi zimatuluka mkatimo ndipo zimaipitsa munthu.”+
21 Pakuti mkatimo, mumtima mwa munthu,+ mumatuluka maganizo oipa. Mumatuluka zadama,*+ zakuba, zaumbanda,+