Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliko 2:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndiponso, palibe munthu amene amathira vinyo watsopano m’matumba achikopa akale. Akachita zimenezo, vinyoyo amaphulitsa matumbawo. Kenako vinyoyo amatayika ndipo matumbawo amawonongeka.+ Koma anthu amathira vinyo watsopano m’matumba achikopa atsopano.”+

  • Luka 5:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Komanso, palibe amene amathira vinyo watsopano m’matumba achikopa akale. Munthu akachita zimenezo, vinyo watsopanoyo amaphulitsa matumba achikopawo.+ Vinyoyo amatayika ndipo matumba achikopawo amawonongeka.+

  • Luka 5:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Koma vinyo watsopano ayenera kuikidwa m’matumba achikopa atsopano.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena