Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 15:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndiyeno kunabwera mayi wina wa ku Foinike+ kuchokera m’zigawo zimenezo ndi kufuula kuti: “Ndichitireni chifundo+ Ambuye, Mwana wa Davide. Mwana wanga wamkazi wagwidwa ndi chiwanda mochititsa mantha.”

  • Mateyu 20:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Iwo anamuyankha kuti: “Ambuye, titseguleni maso athu.”+

  • Aheberi 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chotero, iye anayenera ndithu kukhala ngati “abale” ake m’zonse,+ kuti akhale mkulu wa ansembe wachifundo ndi wokhulupirika pa zinthu za Mulungu.+ Cholinga chake chinali choti apereke nsembe yophimba machimo+ kuti tikhalenso ogwirizana ndi Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena