8 “Chotero ndikukuuzani kuti, Aliyense wovomereza+ pamaso pa anthu kuti ali kumbali yanga, Mwana wa munthunso adzavomereza pamaso pa angelo a Mulungu kuti ali kumbali yake.+
9 Pakuti ngati ukulengeza kwa anthu ‘mawu amene ali m’kamwa mwakowo,’+ akuti Yesu ndiye Ambuye,+ ndipo mumtima mwako ukukhulupirira kuti Mulungu anamuukitsa kwa akufa,+ udzapulumuka.+
5 Choncho amene wapambana pa nkhondo+ adzavekedwa malaya akunja oyera.+ Ndipo sindidzafafaniza dzina lake m’buku la moyo,+ koma ndidzavomereza dzina lake pamaso pa Atate wanga,+ ndi pamaso pa angelo ake.+