Mateyu 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “Chotero aliyense wovomereza pamaso pa anthu kuti ali kumbali yanga, inenso ndidzavomereza+ pamaso pa Atate wanga wakumwamba kuti ndili kumbali yake. Maliko 8:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pakuti aliyense wochita manyazi ndi ine, komanso ndi mawu anga mu m’badwo wachigololo ndi wochimwa uno, Mwana wa munthu adzachitanso naye manyazi+ akadzafika mu ulemerero wa Atate wake limodzi ndi angelo oyera.”+
32 “Chotero aliyense wovomereza pamaso pa anthu kuti ali kumbali yanga, inenso ndidzavomereza+ pamaso pa Atate wanga wakumwamba kuti ndili kumbali yake.
38 Pakuti aliyense wochita manyazi ndi ine, komanso ndi mawu anga mu m’badwo wachigololo ndi wochimwa uno, Mwana wa munthu adzachitanso naye manyazi+ akadzafika mu ulemerero wa Atate wake limodzi ndi angelo oyera.”+