Luka 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo anabereka mwana wake woyamba wamwamuna.+ Anamukulunga ndi nsalu n’kumugoneka modyeramo ziweto,+ chifukwa anasowa malo m’nyumba ya alendo.
7 Ndipo anabereka mwana wake woyamba wamwamuna.+ Anamukulunga ndi nsalu n’kumugoneka modyeramo ziweto,+ chifukwa anasowa malo m’nyumba ya alendo.