Mateyu 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma sanagone+ naye mpaka anabereka mwana wamwamuna.+ Mwanayo anamutcha dzina lakuti Yesu.+