Yeremiya 31:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Yehova wanena kuti, ‘Mawu amveka ku Rama.+ Kwamveka kulira mofuula ndiponso momvetsa chisoni.+ Rakele+ akulirira ana ake.+ Iye wakana kutonthozedwa pamene akulirira ana ake,+ chifukwa ana akewo kulibenso.’”+ Yeremiya 31:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova wanena kuti: “‘Tonthola, usalire. Usagwetsenso misozi,+ pakuti ulandira mphoto ya ntchito zako,’ watero Yehova, ‘ndipo anawo adzabwerera kuchokera kudziko la mdani.’+
15 “Yehova wanena kuti, ‘Mawu amveka ku Rama.+ Kwamveka kulira mofuula ndiponso momvetsa chisoni.+ Rakele+ akulirira ana ake.+ Iye wakana kutonthozedwa pamene akulirira ana ake,+ chifukwa ana akewo kulibenso.’”+
16 Yehova wanena kuti: “‘Tonthola, usalire. Usagwetsenso misozi,+ pakuti ulandira mphoto ya ntchito zako,’ watero Yehova, ‘ndipo anawo adzabwerera kuchokera kudziko la mdani.’+