Rute 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano uwu ndiwo mzere wa mbadwa za Perezi:+ Perezi anabereka Hezironi,+ Luka 3:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 mwana wa Aminadabu,+mwana wa Arini,+mwana wa Hezironi,+mwana wa Perezi,+mwana wa Yuda,+