Maliko 7:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yesu atamva mawuwo anauza mayiyo kuti: “Chifukwa wanena zimenezi, pita, chiwandacho chatuluka mwa mwana wakoyo.”+ Yohane 4:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Pamenepo bamboyo anadziwa kuti linali ola lomwelo+ pamene Yesu anamuuza kuti: “Mwana wako ali moyo.” Ndipo iye ndi banja lake lonse anakhulupirira.+
29 Yesu atamva mawuwo anauza mayiyo kuti: “Chifukwa wanena zimenezi, pita, chiwandacho chatuluka mwa mwana wakoyo.”+
53 Pamenepo bamboyo anadziwa kuti linali ola lomwelo+ pamene Yesu anamuuza kuti: “Mwana wako ali moyo.” Ndipo iye ndi banja lake lonse anakhulupirira.+