Mateyu 23:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Njoka inu, ana a mphiri,+ mudzathawa bwanji chiweruzo cha Gehena?+ Luka 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo anayamba kuuza khamu la anthu obwera kwa iye kudzabatizidwa kuti: “Ana a njoka inu,+ ndani wakuchenjezani kuti muthawe mkwiyo umene ukubwerawo?+ Luka 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsoka kwa akazi apakati ndi kwa oyamwitsa ana m’masiku amenewo!+ Pakuti m’dzikoli mudzakhala mavuto aakulu ndi mkwiyo pa anthu awa. Aroma 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma chifukwa chakuti ndiwe wosafuna kusintha khalidwe+ ndiponso wa mtima wosalapa,+ ukudzisungira mkwiyo wa Mulungu.+ Mulungu adzasonyeza mkwiyo+ umenewu pa tsiku loulula+ chiweruzo chake cholungama.+ Chivumbulutso 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 chifukwa tsiku lalikulu+ la mkwiyo wawo+ lafika, ndipo ndani angaimirire pamaso pawo?”+
7 Pamenepo anayamba kuuza khamu la anthu obwera kwa iye kudzabatizidwa kuti: “Ana a njoka inu,+ ndani wakuchenjezani kuti muthawe mkwiyo umene ukubwerawo?+
23 Tsoka kwa akazi apakati ndi kwa oyamwitsa ana m’masiku amenewo!+ Pakuti m’dzikoli mudzakhala mavuto aakulu ndi mkwiyo pa anthu awa.
5 Koma chifukwa chakuti ndiwe wosafuna kusintha khalidwe+ ndiponso wa mtima wosalapa,+ ukudzisungira mkwiyo wa Mulungu.+ Mulungu adzasonyeza mkwiyo+ umenewu pa tsiku loulula+ chiweruzo chake cholungama.+