Luka 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho anayamba kuuza gulu la anthu amene ankabwera kwa iye kudzabatizidwa kuti: “Ana a njoka inu, ndi ndani wakuchenjezani kuti muthawe mkwiyo umene ukubwerawo?+
7 Choncho anayamba kuuza gulu la anthu amene ankabwera kwa iye kudzabatizidwa kuti: “Ana a njoka inu, ndi ndani wakuchenjezani kuti muthawe mkwiyo umene ukubwerawo?+