2 Timoteyo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tikapitiriza kupirira, tidzalamuliranso limodzi ndi iye monga mafumu.+ Tikamukana,+ iyenso adzatikana, Chivumbulutso 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 n’kutipanga kukhala mafumu+ ndi ansembe+ kwa Mulungu wake ndi Atate wake, kwa iyeyo kukhale ulemerero ndi mphamvu kwamuyaya.+ Ame.
12 Tikapitiriza kupirira, tidzalamuliranso limodzi ndi iye monga mafumu.+ Tikamukana,+ iyenso adzatikana,
6 n’kutipanga kukhala mafumu+ ndi ansembe+ kwa Mulungu wake ndi Atate wake, kwa iyeyo kukhale ulemerero ndi mphamvu kwamuyaya.+ Ame.