Mateyu 25:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Mwana wa munthu+ akadzafika mu ulemerero wake, limodzi ndi angelo ake onse,+ adzakhala pampando wake wachifumu waulemerero.+ 2 Atesalonika 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi imene Ambuye Yesu adzaonekere*+ kuchokera kumwamba limodzi ndi angelo ake amphamvu+ m’moto walawilawi, inuyo amene panopo mukuvutika mudzapeza mpumulo pamodzi nafe.
31 “Mwana wa munthu+ akadzafika mu ulemerero wake, limodzi ndi angelo ake onse,+ adzakhala pampando wake wachifumu waulemerero.+
7 Pa nthawi imene Ambuye Yesu adzaonekere*+ kuchokera kumwamba limodzi ndi angelo ake amphamvu+ m’moto walawilawi, inuyo amene panopo mukuvutika mudzapeza mpumulo pamodzi nafe.