Mateyu 12:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Amene sali kumbali yanga ndi wotsutsana ndi ine, ndipo amene sagwira limodzi ndi ine ntchito yosonkhanitsa anthu kwa ine amawabalalitsa.+ Luka 9:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Koma Yesu anamuuza kuti: “Musamuletse amuna inu, chifukwa amene sakutsutsana nanu ali kumbali yanu.”+ Luka 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Amene sali kumbali yanga akutsutsana ndi ine, ndipo amene sasonkhanitsa anthu pamodzi ndi ine amawabalalitsa.+
30 Amene sali kumbali yanga ndi wotsutsana ndi ine, ndipo amene sagwira limodzi ndi ine ntchito yosonkhanitsa anthu kwa ine amawabalalitsa.+
50 Koma Yesu anamuuza kuti: “Musamuletse amuna inu, chifukwa amene sakutsutsana nanu ali kumbali yanu.”+
23 Amene sali kumbali yanga akutsutsana ndi ine, ndipo amene sasonkhanitsa anthu pamodzi ndi ine amawabalalitsa.+