Mateyu 12:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Amene sali kumbali yanga ndi wotsutsana ndi ine, ndipo amene sagwira limodzi ndi ine ntchito yosonkhanitsa anthu kwa ine amawabalalitsa.+ Maliko 9:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Pakuti amene sakutsutsana ndi ife ali kumbali yathu.+ Luka 9:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Koma Yesu anamuuza kuti: “Musamuletse amuna inu, chifukwa amene sakutsutsana nanu ali kumbali yanu.”+ Yohane 11:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Ndipo osati kufera mtundu chabe, komanso kuti asonkhanitse pamodzi+ ana a Mulungu obalalika.+
30 Amene sali kumbali yanga ndi wotsutsana ndi ine, ndipo amene sagwira limodzi ndi ine ntchito yosonkhanitsa anthu kwa ine amawabalalitsa.+
50 Koma Yesu anamuuza kuti: “Musamuletse amuna inu, chifukwa amene sakutsutsana nanu ali kumbali yanu.”+