Salimo 110:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 110 Yehova wauza Ambuye wanga kuti:+“Khala kudzanja langa lamanja+Kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako.”+ Aefeso 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 imene waigwiritsa ntchito pa Khristu pamene anamuukitsa kwa akufa+ ndi kumukhazika kudzanja lake lamanja+ m’malo akumwamba.+ Akolose 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komabe, ngati munaukitsidwa+ limodzi ndi Khristu, pitirizani kufuna zinthu zakumwamba,+ kumene Khristu wakhala kudzanja lamanja la Mulungu.+
110 Yehova wauza Ambuye wanga kuti:+“Khala kudzanja langa lamanja+Kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako.”+
20 imene waigwiritsa ntchito pa Khristu pamene anamuukitsa kwa akufa+ ndi kumukhazika kudzanja lake lamanja+ m’malo akumwamba.+
3 Komabe, ngati munaukitsidwa+ limodzi ndi Khristu, pitirizani kufuna zinthu zakumwamba,+ kumene Khristu wakhala kudzanja lamanja la Mulungu.+