Salimo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,+Ndipo nduna zapamwamba zasonkhana pamodzi mogwirizana.+Atero kuti alimbane ndi Yehova+ komanso wodzozedwa wake.+ Machitidwe 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo, ndipo olamulira asonkhana pamodzi mogwirizana, kuti alimbane ndi Yehova komanso wodzozedwa wake.’+
2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,+Ndipo nduna zapamwamba zasonkhana pamodzi mogwirizana.+Atero kuti alimbane ndi Yehova+ komanso wodzozedwa wake.+ Machitidwe 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo, ndipo olamulira asonkhana pamodzi mogwirizana, kuti alimbane ndi Yehova komanso wodzozedwa wake.’+
26 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo, ndipo olamulira asonkhana pamodzi mogwirizana, kuti alimbane ndi Yehova komanso wodzozedwa wake.’+