Mateyu 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano Yesu anaimirira pamaso pa bwanamkubwa, ndipo bwanamkubwayo anamufunsa kuti: “Kodi ndiwe mfumu ya Ayuda?”+ Yesu anayankha kuti: “Mukunena nokha.”+ Luka 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano Pilato anamufunsa funso kuti: “Kodi ndiwe mfumu ya Ayuda?” Pomuyankha iye anati: “Mukunena nokha.”+
11 Tsopano Yesu anaimirira pamaso pa bwanamkubwa, ndipo bwanamkubwayo anamufunsa kuti: “Kodi ndiwe mfumu ya Ayuda?”+ Yesu anayankha kuti: “Mukunena nokha.”+
3 Tsopano Pilato anamufunsa funso kuti: “Kodi ndiwe mfumu ya Ayuda?” Pomuyankha iye anati: “Mukunena nokha.”+