Mateyu 26:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma ndikadzauka kwa akufa, ndidzatsogola kukafika ku Galileya inu musanafikeko.”+ Mateyu 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo pitani mwamsanga mukauze ophunzira ake kuti wauka kwa akufa,+ moti padakali pano, watsogola kupita ku Galileya.+ Kumeneko mukamuona. Umenewutu ndi uthenga wanga kwa inu.”+
7 Ndipo pitani mwamsanga mukauze ophunzira ake kuti wauka kwa akufa,+ moti padakali pano, watsogola kupita ku Galileya.+ Kumeneko mukamuona. Umenewutu ndi uthenga wanga kwa inu.”+