Yesaya 63:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Inutu ndinu Atate wathu.+ Ngakhale kuti Abulahamu sanatidziwe ndipo Isiraeli sanatizindikire, inuyo Yehova ndinu Atate wathu. Dzina lanu ndinu Wotiwombola wakalekale.+ Mateyu 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma ndikukutsimikizirani kuti ambiri ochokera kum’mawa ndi kumadzulo+ adzabwera ndi kukhala patebulo limodzi ndi Abulahamu, Isaki ndi Yakobo mu ufumu+ wakumwamba,+
16 Inutu ndinu Atate wathu.+ Ngakhale kuti Abulahamu sanatidziwe ndipo Isiraeli sanatizindikire, inuyo Yehova ndinu Atate wathu. Dzina lanu ndinu Wotiwombola wakalekale.+
11 Koma ndikukutsimikizirani kuti ambiri ochokera kum’mawa ndi kumadzulo+ adzabwera ndi kukhala patebulo limodzi ndi Abulahamu, Isaki ndi Yakobo mu ufumu+ wakumwamba,+