Mateyu 26:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Zoona, Mwana wa munthu akuchokadi, monga Malemba amanenera+ za iye, koma tsoka+ kwa munthu amene akupereka Mwana wa munthu!+ Zikanakhala bwino munthu ameneyu akanapanda kubadwa.” Yuda 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsoka kwa iwo, chifukwa chakuti ayenda m’njira ya Kaini.+ Athamangira m’njira yolakwika ya Balamu+ kuti alandire mphoto, ndipo awonongeka potengera kulankhula kopanduka+ kwa Kora.+ Chivumbulutso 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Koma ngakhale zili choncho, ndakupeza ndi milandu ingapo. Iwe kumeneko uli ndi anthu olimbikira chiphunzitso cha Balamu,+ amene anaphunzitsa Balaki+ kuikira ana a Isiraeli chopunthwitsa kuti adye zoperekedwa nsembe kwa mafano ndi kuchita dama.+
24 Zoona, Mwana wa munthu akuchokadi, monga Malemba amanenera+ za iye, koma tsoka+ kwa munthu amene akupereka Mwana wa munthu!+ Zikanakhala bwino munthu ameneyu akanapanda kubadwa.”
11 Tsoka kwa iwo, chifukwa chakuti ayenda m’njira ya Kaini.+ Athamangira m’njira yolakwika ya Balamu+ kuti alandire mphoto, ndipo awonongeka potengera kulankhula kopanduka+ kwa Kora.+
14 “‘Koma ngakhale zili choncho, ndakupeza ndi milandu ingapo. Iwe kumeneko uli ndi anthu olimbikira chiphunzitso cha Balamu,+ amene anaphunzitsa Balaki+ kuikira ana a Isiraeli chopunthwitsa kuti adye zoperekedwa nsembe kwa mafano ndi kuchita dama.+