Mateyu 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamene Yesu anali kudutsa kuchokera kumeneko, anthu awiri akhungu+ anam’tsatira. Iwo anafuula ndi kunena kuti: “Mutichitire chifundo,+ Mwana wa Davide.” Mateyu 20:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno amuna awiri akhungu anakhala pansi m’mphepete mwa msewu ndipo atamva kuti Yesu akudutsa, anafuula kuti: “Ambuye, Mwana wa Davide, tichitireni chifundo!”+
27 Pamene Yesu anali kudutsa kuchokera kumeneko, anthu awiri akhungu+ anam’tsatira. Iwo anafuula ndi kunena kuti: “Mutichitire chifundo,+ Mwana wa Davide.”
30 Ndiyeno amuna awiri akhungu anakhala pansi m’mphepete mwa msewu ndipo atamva kuti Yesu akudutsa, anafuula kuti: “Ambuye, Mwana wa Davide, tichitireni chifundo!”+