31 Kenako, anayamba kuwaphunzitsa kuti Mwana wa munthu ayenera kukumana ndi mavuto ambiri. Iye adzakanidwa ndi akulu, ansembe aakulu ndi alembi. Ndiyeno adzaphedwa,+ koma adzauka patapita masiku atatu.+
31 Pakuti anali kuphunzitsa ophunzira ake ndi kuwauza kuti: “Mwana wa munthu adzaperekedwa m’manja mwa anthu, ndipo adzamupha,+ koma ngakhale adzamuphe, adzauka patapita masiku atatu.”+
22 Kenako anati: “Mwana wa munthu ayenera kukumana ndi mavuto ambiri. Iye adzakanidwa ndi akulu, ansembe aakulu ndi alembi. Ndiyeno adzaphedwa,+ koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+