Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 22:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mphamvu yanga yauma gwaa, ngati phale.+

      Lilime langa lamamatira kunkhama zanga,+

      Ndipo mwandikhazika m’fumbi la imfa.+

  • Yesaya 53:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Iye anabayidwa+ chifukwa cha zolakwa zathu.+ Anaphwanyidwa chifukwa cha zochimwa zathu.+ Chilango chotibweretsera mtendere chinam’gwera iyeyo,+ ndipo chifukwa cha zilonda zake+ ifeyo tachiritsidwa.+

  • Yesaya 53:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Iye anaponderezedwa ndipo anatengedwa popanda kuweruzidwa mwachilungamo.+ Ndani amene anaganizira tsatanetsatane wa mibadwo ya makolo ake?+ Pakuti iye anadulidwa+ m’dziko la amoyo.+ Chifukwa cha zolakwa+ za anthu anga, iye anakwapulidwa.+

  • Danieli 11:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Iye adzagonjetsa magulu ankhondo+ okhala ngati madzi osefukira, ndipo magulu ankhondowo adzawonongedwa.+ Mtsogoleri+ wa pangano+ nayenso+ adzawonongedwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena