Genesis 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Nowa analowa m’chingalawacho, limodzi ndi ana ake aamuna, mkazi wake, ndi akazi a ana ake. Iwo analowamo madzi achigumula asanayambe.+ Mateyu 24:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 M’masiku amenewo chigumula chisanafike, anthu anali kudya ndi kumwa. Amuna anali kukwatira ndipo akazi anali kukwatiwa, kufikira tsiku limene Nowa+ analowa m’chingalawa.+
7 Pamenepo Nowa analowa m’chingalawacho, limodzi ndi ana ake aamuna, mkazi wake, ndi akazi a ana ake. Iwo analowamo madzi achigumula asanayambe.+
38 M’masiku amenewo chigumula chisanafike, anthu anali kudya ndi kumwa. Amuna anali kukwatira ndipo akazi anali kukwatiwa, kufikira tsiku limene Nowa+ analowa m’chingalawa.+