Yohane 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno khamu la anthulo litaona kuti Yesu komanso ophunzira ake kulibe, linakwera ngalawa zawo zing’onozing’ono ndi kupita ku Kaperenao kukafunafuna+ Yesu. Yohane 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amenewa anafika kwa Filipo+ wa ku Betsaida ku Galileya, ndipo anayamba kumupempha kuti: “Bambo, ife tikufuna kuona Yesu.”+
24 Ndiyeno khamu la anthulo litaona kuti Yesu komanso ophunzira ake kulibe, linakwera ngalawa zawo zing’onozing’ono ndi kupita ku Kaperenao kukafunafuna+ Yesu.
21 Amenewa anafika kwa Filipo+ wa ku Betsaida ku Galileya, ndipo anayamba kumupempha kuti: “Bambo, ife tikufuna kuona Yesu.”+