Luka 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zakeyu anali kufunitsitsa kuona+ Yesu kuti ndi wotani, koma sanathe kutero chifukwa cha khamu la anthu, pakuti anali wamfupi. Luka 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Herode ataona Yesu anakondwera kwambiri, chifukwa kwa nthawi yaitali ndithu anali kufunitsitsa kuti amuone+ popeza anali kumva+ za iye. Komanso anali kuyembekezera kuona chizindikiro chimene iye angachite.
3 Zakeyu anali kufunitsitsa kuona+ Yesu kuti ndi wotani, koma sanathe kutero chifukwa cha khamu la anthu, pakuti anali wamfupi.
8 Herode ataona Yesu anakondwera kwambiri, chifukwa kwa nthawi yaitali ndithu anali kufunitsitsa kuti amuone+ popeza anali kumva+ za iye. Komanso anali kuyembekezera kuona chizindikiro chimene iye angachite.