Mateyu 24:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Inunso chimodzimodzi, mukadzaona zinthu zonsezi, mudzadziwe kuti iye ali pafupi, ali pakhomo penipeni.+ Luka 17:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Afarisi atamufunsa kuti ufumu wa Mulungu udzabwera liti,+ iye anawayankha kuti: “Ufumu wa Mulungu sudzabwera mwa maonekedwe ochititsa chidwi ayi. Machitidwe 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano atasonkhana pamodzi, anayamba kumufunsa kuti: “Ambuye, kodi mubwezeretsa ufumu+ kwa Isiraeli pa nthawi ino?” 2 Atesalonika 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kuti musafulumire kugwedezeka pa maganizo anu, kapena kutengekatengeka ndi mawu ouziridwa+ onena kuti tsiku la Yehova lafika.+ Musatero ayi, ngakhale utakhala uthenga wapakamwa,+ kapena kalata+ yooneka ngati yachokera kwa ife.
33 Inunso chimodzimodzi, mukadzaona zinthu zonsezi, mudzadziwe kuti iye ali pafupi, ali pakhomo penipeni.+
20 Tsopano Afarisi atamufunsa kuti ufumu wa Mulungu udzabwera liti,+ iye anawayankha kuti: “Ufumu wa Mulungu sudzabwera mwa maonekedwe ochititsa chidwi ayi.
6 Tsopano atasonkhana pamodzi, anayamba kumufunsa kuti: “Ambuye, kodi mubwezeretsa ufumu+ kwa Isiraeli pa nthawi ino?”
2 kuti musafulumire kugwedezeka pa maganizo anu, kapena kutengekatengeka ndi mawu ouziridwa+ onena kuti tsiku la Yehova lafika.+ Musatero ayi, ngakhale utakhala uthenga wapakamwa,+ kapena kalata+ yooneka ngati yachokera kwa ife.