Mateyu 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho amene analandira matalente asanu uja anabwera ndi matalente ena owonjezera asanu, n’kunena kuti, ‘Ambuye, paja munandipatsa matalente asanu koma onani, ndapindula matalente enanso asanu.’+
20 Choncho amene analandira matalente asanu uja anabwera ndi matalente ena owonjezera asanu, n’kunena kuti, ‘Ambuye, paja munandipatsa matalente asanu koma onani, ndapindula matalente enanso asanu.’+