Luka 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Woyamba anafika ndipo ananena kuti, ‘Mbuyanga, ndalama yanu ya mina ija inapindula ndalama zina 10 za mina.’+
16 Woyamba anafika ndipo ananena kuti, ‘Mbuyanga, ndalama yanu ya mina ija inapindula ndalama zina 10 za mina.’+