Maliko 12:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Davideyo anamutcha kuti ‘Ambuye,’ nanga zikutheka bwanji kuti alinso mwana wake?”+ Ndipo khamu lalikulu linali kumumvetsera mosangalala.+ Luka 21:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndipo anthu onse+ anali kulawirira m’mawa kwambiri kupita kwa iye kukachisi kuti akamumvetsere.
37 Davideyo anamutcha kuti ‘Ambuye,’ nanga zikutheka bwanji kuti alinso mwana wake?”+ Ndipo khamu lalikulu linali kumumvetsera mosangalala.+