Mateyu 21:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anatumizanso akapolo ena ambiri kuposa oyamba aja, koma amenewa anawachitanso chimodzimodzi.+ Maliko 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye anatumizanso kapolo wina kwa iwo koma ameneyu anamutema m’mutu ndi kumuchitira zachipongwe.+