Mateyu 21:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Alimiwo ataona mwanayo anayamba kukambirana kuti, ‘Eya, uyu ndiye wolandira cholowa.+ Bwerani, tiyeni timuphe ndi kutenga cholowa chakecho!’+ Maliko 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma alimiwo anayamba kukambirana kuti, ‘Eya, uyu ndiye wolandira cholowa.+ Bwerani, tiyeni timuphe, ndipo cholowacho chidzakhala chathu.’+
38 Alimiwo ataona mwanayo anayamba kukambirana kuti, ‘Eya, uyu ndiye wolandira cholowa.+ Bwerani, tiyeni timuphe ndi kutenga cholowa chakecho!’+
7 Koma alimiwo anayamba kukambirana kuti, ‘Eya, uyu ndiye wolandira cholowa.+ Bwerani, tiyeni timuphe, ndipo cholowacho chidzakhala chathu.’+