Mateyu 21:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Iwo anayankha kuti: “Chifukwa chakuti ndi oipa, adzawawononga koopsa+ ndipo munda wa mpesawo adzaupereka kwa alimi ena, amene angam’patse zipatso m’nyengo yake.”+ Maliko 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi mwinimunda wa mpesawo adzachita chiyani? Adzabwera ndi kupha alimiwo, ndipo munda wa mpesawo+ adzaupereka kwa ena.+
41 Iwo anayankha kuti: “Chifukwa chakuti ndi oipa, adzawawononga koopsa+ ndipo munda wa mpesawo adzaupereka kwa alimi ena, amene angam’patse zipatso m’nyengo yake.”+
9 Kodi mwinimunda wa mpesawo adzachita chiyani? Adzabwera ndi kupha alimiwo, ndipo munda wa mpesawo+ adzaupereka kwa ena.+