Mateyu 21:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Tsopano ansembe aakulu ndi Afarisi atamvetsera mafanizo akewa, anazindikira kuti anali kunena za iwo.+ Maliko 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atamva zimenezo anayamba kufunafuna njira yomugwirira, koma anaopa khamu la anthu, pakuti iwo anazindikira kuti iye ananena fanizolo akuganiza za iwowo. Choncho anangomusiya n’kuchokapo.+
45 Tsopano ansembe aakulu ndi Afarisi atamvetsera mafanizo akewa, anazindikira kuti anali kunena za iwo.+
12 Atamva zimenezo anayamba kufunafuna njira yomugwirira, koma anaopa khamu la anthu, pakuti iwo anazindikira kuti iye ananena fanizolo akuganiza za iwowo. Choncho anangomusiya n’kuchokapo.+