Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 19:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “‘Musamaweruze mopanda chilungamo. Musamakondere munthu wosauka,+ ndiponso musamakondere munthu wolemera.+ Mnzako uzimuweruza mwachilungamo.

  • Mateyu 22:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Choncho anamutumizira ophunzira awo, limodzi ndi achipani cha Herode,+ ndipo iwo anati: “Mphunzitsi, tikudziwa kuti inu mumanena zoona ndipo mumaphunzitsa njira ya Mulungu m’choonadi, ndiponso simusamala kuti uyu ndani, chifukwa simuyang’ana maonekedwe a anthu.+

  • Maliko 12:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Atafika, iwo anamuuza kuti: “Mphunzitsi, tikudziwa kuti inu mumanena zoona ndipo simusamala kuti uyu ndani, chifukwa simuyang’ana maonekedwe a munthu, koma mumaphunzitsa njira ya Mulungu mogwirizana ndi choonadi:+ Kodi n’kololeka kupereka msonkho kwa Kaisara kapena ayi?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena