Miyambo 26:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu wodana nawe amadzibisa ndi milomo yake, koma mkati mwake mumakhala chinyengo.+ Mateyu 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Yesu, podziwa kuipa mtima kwawo, ananena kuti: “Onyenga inu! Bwanji mukundiyesa?+ Maliko 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi tizipereka kapena tisamapereke?”+ Pozindikira chinyengo chawo, Yesu anawafunsa kuti: “Bwanji mukundiyesa? Bweretsani khobidi la dinari kuno ndilione.”+
15 Kodi tizipereka kapena tisamapereke?”+ Pozindikira chinyengo chawo, Yesu anawafunsa kuti: “Bwanji mukundiyesa? Bweretsani khobidi la dinari kuno ndilione.”+