Mateyu 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno anawafunsa kuti: “Kodi nkhope iyi ndi mawu akewa n’zandani?”+ Maliko 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwo anam’patsadi. Ndipo iye anawafunsa kuti: “Kodi chifaniziro ichi ndi mawu akewa n’zandani?” Iwo anayankha kuti: “Ndi za Kaisara.”+
16 Iwo anam’patsadi. Ndipo iye anawafunsa kuti: “Kodi chifaniziro ichi ndi mawu akewa n’zandani?” Iwo anayankha kuti: “Ndi za Kaisara.”+